| Always | Nthawi zonse |
| I always wanted to marry you | Nthawi zones ndakhala ndikufuna kukwatila iwe |
| Never | Kukana kuchitanso |
| I will never do this again! | Sindizachitanso zimenezi |
| Now | Pano |
| We have to leave now! | Tikuyenela kunyamuka pano! |
| Sometimes | Nthawi zina |
| Sometimes I prefer to be at home | Nthawi zina ndimasankha kukhala pakhomo |
| Nthawi zambiri | Mara kwa mara |
| From time to time I eat rice | Nthawi zambiri ndimadya mpunga |
| Late | Kuchedwa |
| The bus is always late | Basi imachedwa nthawi zambiri |
| Later | Nthawi yina |
| The bus will come later | Basi yibwela nthawi ina |
| Early | Mwansanga |
| You should try to come home early | 1) Udziyesesa kubwela pakhomo mwansanga 2) (formal) Mudziyesesa kubwela pakhomo mwansanga |
