| Where? | Kuti? |
| Where is Shaik's house? | Nyumba ya Shaik ili kuti? |
| Where is this? | Kuti kumeneko? |
| When? | Liti? |
| When is George coming? | Mialy abwela liti? |
| When will you travel? | Upita liti? |
| How? | Bwanji? |
| How can I get to Mangochi? | Ndingafike bwanji ku Mangochi? |
| How is your brother? | 1) Mlongo wako ali bwanji? 2) (formal) Mlongo wanu ali bwanji? |
| Which? | 1) Chiti (sin.) 2) Ati & Ziti (plu.) |
| Which land is mine? | Malo anga ndi ati? |
| What? | Chiyani? |
| What did you do? ? | Wachita chiyani? |
| Who? | Ndani? |
| Who is the traditional leader of this village? | Mfumu ya mudzi uni ndi ndani? |
| Who did this? | Anachita izi ndi ndani? |
| Why? | Chifukwa? |
| Why did he do this? | Anachita izi chifukwa chiyani? |
| Why is there no food | Ndi chifukwa chiyani palibe chakudya? |
