| What day is today? | Ndi tsiku lanji lero? |
| Monday | Lolemba |
| Tuesday | Lachiwiri |
| Wednesday | Lachitatu |
| Thursday | Lachinayi |
| Friday | Lachisanu |
| Saturday | Loweluka |
| Sunday | Lamulungu |
| What day is today? | Ndi tsiku lanji lero? |
| Monday | Lolemba |
| Tuesday | Lachiwiri |
| Wednesday | Lachitatu |
| Thursday | Lachinayi |
| Friday | Lachisanu |
| Saturday | Loweluka |
| Sunday | Lamulungu |
| This week | 1) Sabata ino 2) Mulungu uno |
| I have exam on Friday this week | 1) Ndili ndi mayeso lachisanu sabata ino 2) Ndili ndi mayeso lachisanu mulungu uno |
| Next week | 1) Sabata yamawa 2) Mulungu wamawa |
| I will return next week Saturday | 1) Ndibwelako loweluka sabata yamawa 2) Ndibwelako loweluka mulungu wamawa |
| Last week | 1) Sabata yatha 2) Mulungu watha |
| She went shopping last week Monday | Anapita kokagula zinthu lolemba lapitali |
| I need to travel to Nairobi on Tuesday because I have another flight on the same day and I would arrive in the Dubai on the following Wednesday | Ndifukuna kupita ku Nairobi lachiwiri chifukwa ndikuyenela kukakwela ndege tsiku lomweli kuti ndikafike ku Dubai lachitatu |
West Africa- Ìgbò - Wolof - Yorùbá |
East Africa- Chichewa (Nyanja) - Kinyarwanda (Ikinyarwanda) - Kiswahili |
Central Africa- Chokwe (Wuchokwe) - Ibinda (Fiote) - Kikongo - Lingala - Tshiluba |
Southern Africa- Malagasy - Naro (Senaro) - Nyaneka-Humbi - Sekaukau - Setswana (Tswana) - Shona (chiShona) - Umbundu (South Mbundu) - IsiXhosa (Xhosa) - IsiZulu (Zulu) |