Chichewa Language


Days of the week in Chichewa

What day is today? Ndi tsiku lanji lero?
Monday Lolemba
Tuesday Lachiwiri
Wednesday Lachitatu
Thursday Lachinayi
Friday Lachisanu
Saturday Loweluka
Sunday Lamulungu

How to describe weeks

This week 1) Sabata ino
2) Mulungu uno
I have exam on Friday this week 1) Ndili ndi mayeso lachisanu sabata ino
2) Ndili ndi mayeso lachisanu mulungu uno
Next week 1) Sabata yamawa
2) Mulungu wamawa
I will return next week Saturday 1) Ndibwelako loweluka sabata yamawa
2) Ndibwelako loweluka mulungu wamawa
Last week 1) Sabata yatha
2) Mulungu watha
She went shopping last week Monday Anapita kokagula zinthu lolemba lapitali

A sample sentence

I need to travel to Nairobi on Tuesday because I have another flight on the same day and I would arrive in the Dubai on the following Wednesday Ndifukuna kupita ku Nairobi lachiwiri chifukwa ndikuyenela kukakwela ndege tsiku lomweli kuti ndikafike ku Dubai lachitatu

Learn Chichewa

------
African Languages on Mofeko

West Africa


- Ìgbò
- Wolof
- Yorùbá

East Africa


- Chichewa (Nyanja)
- Kinyarwanda (Ikinyarwanda)
- Kiswahili

Central Africa


- Chokwe (Wuchokwe)
- Ibinda (Fiote)
- Kikongo
- Lingala
- Tshiluba

Southern Africa


- Malagasy
- Naro (Senaro)
- Nyaneka-Humbi
- Sekaukau
- Setswana (Tswana)
- Shona (chiShona)
- Umbundu (South Mbundu)
- IsiXhosa (Xhosa)
- IsiZulu (Zulu)